Odwala wadzikhwezera muchimbudzi cha pachipatala
Bambo wina wa zaka 37 yemwe amalandira thandizo la mankhwala pa chipatala cha Mzuzu Central wadzipha podzimangilira m'chimbudzi cha pa chipatalapo. Watsimikiza za nkhaniyi ndi oyankhulira chipatala cha Mzuzu Central a Anord Kayira omwe azindikira… ...