Watiyankhulira bwino: A Malawi lekani kuika oyimba pa mpikisano – Lucius Banda watayira ka mtengo Namadingo
Chiyamba kale pa maimbidwe Lucius Banda watayira ka mtengo oyimba wamakono, Patience Namadingo, poyankhula zakupsa posachedwapa koma wadzudzula anthu mdziko muno kuti asiye mchitidwe oyika oyimba pa mpikisano. Izi zili mu uthenga omwe Banda wayika… ...