Nepman to release Amapiano song
Oyimba Nepman yemwe dzina lake lenileni ndi Neppier Longwe wadzudzula oyimba anzake omwe akumaonetsera mkhalidwe wa nsanje mmayimbidwe a m'dziko muno. Nepman, yemwe padakali pano ali m'dziko la Zambia wayankhula chomwechi kudzera pa tsamba lake… ...