Chilima zamvuta, atha osaima 2019
....tikamangala, yatero UTM Pali chiopsezo choti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima atha osapikisana nawo paudindo wa mtsogoleri wa dziko lino pa chisankho cha patatu chomwe chitachitike chaka mawa chino. Izi zikutsatira… ...