Iwalani kaye za Konveshoni – Chakwera
A Kongeresi kodi mulipo apa? Musapite kutali chifukwa tili ndi uthenga wanu. Zija za Konveshoni mumadikila zija kuti ichitika lero pa 5, ku Mzuzu, ati muziiwale kaye. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha MCP, a Lazarus… ...