
Luso lamakono ndilofunika pokwanilitsa masomphenya achitukuko a 2063 – Theu
Boma lati liri ndichidwi komaso likufuna kuti dziko lino likhale patsogolo pa ntchito za luso lamakono, pofuna kukwanitsa masomphenya a chitukuko a 2063. Mmodzi mwa akuluakulu oyang'anila za luso lamakono ku bungwe laboma la Electricity… ...