Kaya wina afune, kaya asafune, 2025 ndikubweleranso m’boma – APM
Inu nonse amene a Peter Mutharika simukuwafuna, yang'anani kumbali. Nonse aja olemba kuti "APM my vote", senderani chifupi. A Mutharika lero abwerezanso kuti chaka cha mawa akubwelera ku Sanjika. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha DPP… ...