Katelele Ching’oma watisiya
M'modzi mwa oyimba odziwika bwino kuno ku Malawi, Katelele Ching'oma, watisiya. Oyimbayu wamwalira m'bandakucha wa lero ku chipatala cha Kamuzu Central ku Lilongwe komwe anamutengela. Mchimwene wake wa oyimbayu, a Elvis Ching'oma, wati Katelele amadwala… ...