Ma suti a Bisnowaty autsa mapiri pa chigwa
Phungu wa dera la pakati mu boma la Lilongwe a David Bisnowaty aputa mavunkhomola. A Bisnowaty dzulo lolemba anajambulitsa ndi Mafumu a mu dera lawo ati atatchena ma suti amene Phungu'yo wawagulila. Polemba pa tsamba… ...