Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino Flames lero pa 26 March ikuyembekezereka kuthambitsana ndi Chipolopolo ya m'dziko la Zambia kulimbirana malo achitatu mu 4 Nations Tournament ndipo masewero ake ayamba 2 koloko masana.… ...
Articles By Gracious Zinazi
Timu ya mpira wa manja ya dziko lino, Malawi Queens, ili pa chiopsenzo chosatenga nawo mbali mu mipikisano ina ikuluikulu ya dziko lonse lapansi monga Fast 5 Netball World Series yomwe imaseweredwa ndi matimu 6… ...
Anthu atatu apezeka ndi nthenda yofilitsa maso yomwe muchingerezi imatchedwaconjunctivitis kapena kuti pink eye mu mzinda wa Blantyre. Malingana ndi kalata yomwe atulutsa owona zaumoyo komanso chisamaliro cha anthu m'bomali, ndipo yasainidwa ndi Dr Gift… ...
Mtsogoleri opuma wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progress Party (DPP) Professor Arthur Peter Mutharika akufuna kuyankhula ndi mtundu wa a Malawi komanso mtsogoleri wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa… ...
Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) yalamula nyumba zowulutsa mawu zomwe zimanenerera mpira pomwe zikuonera m'makanena akunja kapena a m'dziko muno kuti zikuyenera kupereka umboni oti zili ndi chilolezo chochita izi pasanathe masiku asanu… ...
Patangopita masiku ochepa kampani ya lamya za m'manja ya Airtel Malawi itakweza mitengo yogulira ma bandulo ake, nayonso TNM yakweza mitengo yake ndi K20 pa K100 iliyonse. Malingana ndi uthenga omwe kampaniyi yatulutsa yati yachita… ...
Police in Mangochi have arrested five men for allegedly stealing cellphones during the Sand Music Festival held in the district over the weekend The incidents occurred from Friday, September 29, to October 1, 2023, at… ...
Representatives of over 13,000 primary school teachers trained under IPTE 15, 16 and 17 yesterday went to Capital Hill in Lilongwe where they wanted to submit their petition demanding the government to recruit them. This… ...
Kutsatira zionetsero zomwe ophunzira aku Mzuzu University anachita dzulo lachisanu, akuluakulu a sukuluyi alamula ophunzira onse kuti achoke pasukuluyi mam'mawa wa lero loweruka. Malingana ndi kalata yomwe akuluakulu a sukuluyi atulutsa, ophunzira sakuloledwa kupezeka pa… ...
The bodies of 6 members of the same family who were involved in an accident at a place called Mbuna in Lilongwe were laid to rest yesterday at Chinsapo 2 in the city. The funeral… ...
Police in Mangochi District have apprehended Abdul Swalley Ibrahim Mbuje, 43, for being found with a common duiker (antelope). The incident occurred on August 28, 2023 at M'baluku Roadblock. Mbuje was intercepted at the said… ...
Police in Lilongwe have arrested four men for jumping into a moving vehicle with intention of stealing Grocery items. According to Lilongwe police spokesperson Hastings Chigalu, the incident has happened this afternoon at the Shoprite… ...
Bwalo la milandu ku Dowa lagamula mayi wa zaka 42, Flora Thom, kukakhala ku ndende kwa chaka ndi miyezi itatu chifukwa chakuba katundu wa m'nyumba ya bwana wake wa ndalama pafupifupi K2 miliyoni. Bwaloli linamva… ...
Lilongwe Water Board (LWB) yati ndiyokhumudwa ndi mchitidwe wa anthu ena omwe amasankha kusanena nsanga za mapaipi amadzi omwe ophulika m'madera momwe akukhala ndicholinga choti azitunga madzi aulele. Izi zikudza pomwe mmadera ena monga Kaliyeka,… ...
Education experts have commended the Ministry of Education and Malawi National Examinations Board (MANEB) for successfully curbing the malpractice of examination leakage and saving millions of taxpayers’ money that might otherwise have been lost through… ...