School Days
Pomwe zafika pano, yemwe sanaonelebe kanema othyakulidwa kwathu konkuno wa ‘School Days', akutengedwa otsalira zedi m'makwalalamu. Kanema uyu wazula mitima ya a Malawi ochuluka ndipo omwe anaphunzira sukulu zogonera konko akumangomwetulira akamaonera kwinaku akuwasimbira ana… ...