Aphunzitsi m'boma la Machinga athamangira ku ofesi ya mkulu wa maphunziro m'bomalo komwe akuti akufuna kupeza mayankho pa ganizo la ofesiyo yokweza ndalama ya welofeya   opanda chidziwitso.  Malingana ndi m’modzi mwa aphunzitsi, yemwe tayankhula naye,… ...