The Human Rights Defenders Coalition (HRDC) has postponed demonstrations which were slated for Wednesday, 28th August to Friday, 30th August due to an order from the Supreme Court of Appeal. On Tuesday, the Supreme court… ...
Gospel rapper Gwamba, has released a video for the hit song "Unatha". Last month, Gwamba, born Duncan Zgambo, recorded and released his single which within a short period was on most people's tongues. In the… ...
Dausi
Chipani cholamula cha Democratic Progressive (DPP) chatsutsa mwa ntu wagalu zoti otsatira chipanichi ndi omwe awotcha nyumba ya mkulu wa bungwe lomenyera ufulu la HRDC a Timothy Mtambo. Nyumba ya a Mtambo komaso galimoto yawo… ...
Hudson Chamasowa
M’modzi mwa anthu opanga ndakatulo m’dziko muno a Hudson Chamasowa apempha boma kuti lilowelerepo pa ntchito yolimbikitsa ndikutukula luso la ulakatuli. Poyankhula ndi nyuzi ino, a Chamasowa anati boma pakali pano likulephera kuvomereza luso la… ...
Wapampando wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) a Timothy Mtambo, alengeza kuti ayamba aimitsa kaye zionetsero pofuna kupereka mpata ku bwalo la milandu lomwe layamba kumva nkhani yokhudza zotsatira… ...