Tomato atha kukhala golide wathu – atelo akatswiri
…boma alipempha kupeza misika yokhazikika Akatswiri a zaulimi ati ngati ulimi wa tomato ungatengedwe bwino komaso ngati pangakhale njira zamakono zosungira tomato, mbewuyi itha kumabweretsa ndalama zakunja zochuluka kuposa fodya yemwe dziko lino limadalira pano.… ...