Police in Lilongwe are keeping in custody a 21-year-old man for raping a three-year-old girl.
According to Kanengo police public relations officer Salome Chibwana, the suspect James Boni sexually abused the girl at a graveyard.
“The incident happened at Mgona and was reported by the mother to the child who said she was busy cooking when she was informed by a friend that her daughter was found at the graveyard,” Chibwana.
The child later disclosed that she was feeling pain in her private parts and when the mother checked her she saw blood on the child’s private parts.
A test at the hospital confirmed that the child was raped.
The suspect was later arrested after being identified by the victim who revealed that the 21 year old man took her to the graveyard where he raped her.
Boni who is expected to appear before court soon comes from Thekerani in Thyolo district.
That is murder case…..
Wuphedwe basi ayse!!!
But why abaleee?
Ngati nizizimba mmmmm anakunamizani.kodi ulibe wako mwana kuti umupange zimenezo?ngati ulibe upeze wako masiku otsiliza kuvomereza nibwino tili pa deport.
Munthu woipa ameneyo…
Satana Ameneyo
Nkhani Nde Zikutuluka,nanga Yawapolice Wagwirira Mwana Wake Kuzomba Ija Bwanji Sikutuluka?
What’s wrong with some Malawian men. Repent and get saved through Jesus Christ of Nazareth.
Just death sentence is enough
Choncho nkumati a police ndioipa akamakuthilani unyolo, zinthu mukuchita kuziamba nokha, ngati khalidwe lako lili lonunkhalo osakangokoka Hule bwanji? chimakgala chili chani? Umfiti? kukhwima? kaduka ugong’oli? Asakusiye ndithu iwe akukakamile basi.
Kkk apo nde ndi Daylactive maula maula tizikamupasila nsima pa window mpaka mwana wa 3 years munaganiza bwanji?
Castration and Life in prison would be appropriate for the monster.
Achta bwino
Mwina anapangana
Malaulo
Mpaka ndasanzatu… Khalidwe lonunkha ngati chimbudzi cha pa nsika
osapana hule bwanji nayeso
Let him die too
Damn! 21 divide by 3,,
Mmmmmm koma ngati ali ma plan nde mwaonjeza nawotu mmmmm mselu bwanji munalibe man? Iii nanuso nde kayatu
Zayambilaso kodi zopusazi????
Mahule onsewa, Bwanji kumanyenga ana?
Nkumanvapo chani pa mwana wa 3 yrs abale ziwanda zake zoyenda ndi miyendotu
Ndipo zoyenda masana mxiih
Satana uyu ooneka ndimaso sistoo
Oterewa ofunika kuwanthira moto
CAN MALAWIAN MALES STOP RAPING YOUNG GIRLS!!!! I AM SICK OF ALL THE RAPE CASES IN MALAWI!
Akanakhala kuti mwanayo ndi mwana waine nkulu ameneyu nkanamugulila nyanga kungomuloza basi amwalilepo osampitisaso kupolisi zachinyengo basi
mwana wazaka zitatu ? kukhwima , chani? ? 3 years kuti umvamo chani monga anafunsira adha ajawo …. akufunika kuphedwa basi .
eee ameneyo nde kumukakamila koma achina chaponda mkumatulutsa pa bero zautsiru basi
Kungodula zilimmusizo asadzachiteso wopusa.
Should be death penalty! Someone did this to my child I would kill them myself! Basi
Wa 3yrs ndimunthu amene mu std 1 amalesedwa kuti aphunzire nawo. Bambo kusankha kugona naye,nthawi yakumdima ndithu.
Koma zinazi misala kapena zizimba? 100 years IHL
Akufunika kumudula ma battery ake awo
Kkkkkkkkkkkk.
Iwe Colie kikiki
Kkkkkkkkk.mwaperekapo maganizo anu nanunso hetiii.kk
Usakwa!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
ufititu anthu otere azinyongeďwa
Its very pathetic,sad ,shameful and total madness.Government should find other punishable means apart from jail sentences,such people like staying in jails coz they enjoy there Edina WaRodney Shaba Mphangela Moyo Angela Fredrick Lukhere Fortunate Watsopano Lambulira Kondwani Mc-Iver Tole Rodney Adrian Shaba Love Wa Benjamin Shaba Benjamin Shaba Grace Jackson
Mmmm ayi zawonjeza,akuyenela chilango chokhwima
Mankwala dasi tu ndi ufiti.
Raping/ defilement??? komanso anthu aonjeza tizingoona zogwilila ana a under age. Pakufunika punishment yayikulu ndinthu.
cut his balls off
Cut him balls then put him 30 years jail
I think its time the law makers revise this law, give it for life ,for these sodomites??
Ziwanda izi
akukulu nyeleyake yotani mpaka 3ye mahule osewa àaaaa kkkkkkiiiii ochipa mahule 250zikumatheka vutukamfusa ndiciani zopusa simwanawake
Chilango choyenela mfiti ameneyu ndikudula katundu akumutumayo, sitikufuna anthu ochititsa manyazi pa Malawi.
Ngati kuli kufunafuna Ka virgin koti mukayambe nokha aponso mwaonjeza,kungovomereza kuti mavirgin anatha basi
Kkkkkkkk kima amuna
Ndizomvetsa chisoni, nkupanda nzeru kotani mpakana mwana wa zaka zitatu? I think he z crazy, and he must suposed 2 receive a red card!
Happiness is all am experiencing now as am posting this about Dr Abuu the man that God has been using to heal people, and I and my Husband are one of them because we are cured from hiv/aids by his medicine, if not for God and Dr Abuu my children would have been orphans today but i thank God and Dr Abuu for saving my life, for those who are passing through the same should call or whatsapp Dr Abuu on whatsapp with his number +2348066454364 OR EMAIL [email protected]
kkkkk my foot, People are aware now, u r late..
Yesterday it was a 7 year boy who was raped today its this girl may we find fortitude in God himself who can teach us were we went wrong
Woza Malawi!
Foolish man.
(RIP) Rest In Prison.
Kupusa akazi kupaka palipose let him face the law.
At size 1 angavale bwanji size 10!!!
Tisamvetu zoti akhothi amulamula miyezi 48 kundende ayi. Uyu koma miyezi 240 basi
The problem is that you aint giving them stiff punishment…..give life imprisonment….30 going up…….osati tima seven years …10years….amunawa satana waakhalira kuzinthu zawozo
Umenewo nde ndimwano mwinanso ochita kubadwa nawo
Napepe achimwemwe….but its too much… dats wy mutiyankhulisa pambali?….three years zooona …mwana wanzako…..atakhala mwana wanga sangakafike wamoyo kupolisi…nzowawa kwambiri chiwewe chamtundu wanji…three years zooona…..dzana anali wa seven years…kubeleka kumawawa kuti wina azangokuonongera mwana kopanda chisoni
Komaso anthufe tisama yembekezere ndende kuti ikoza zithu ma moster tikuwapanga creat tokha azimayi tikuvala mosazilemekeza pomwe tikulera mwana wa mwA muna pakhomo muganiza akapita kunja akakhala ndi khalidwe kwa anthu oti sachibale ake ?
Kapena tinayiwala kuti anthu ena umunthu mulibe
Charity biggins at home
Zimawawa ana adzaka zochepa kupangidwa chipongwe chonchi chifukwa choti munthu wa mkulu wwa mzeru zake kukanikani kuganiza kuti ndi mwana mpaka kuika chikatundu chake
Iwee ndi kape eti….are you telling me kuti mwana wazaka zitatu wamkaz
Are you telling me mwana wa zaka zitatu ndi mzimai……kupusa chani?…….waseven years mnyamata wagwiriridwa ndi mzibabo wa 37….vutoso apa ndi la azimai mwina kuvunda akatundu anuwo….stupid idiot
Shaaah Anakwia Pamela Mpaka Anamenya Tebulo
mmmmm
Akafere Ngt Zili Zoona
umfiti chyani amvapo chyani bvoa wa misala nayeso poti ndi munthu koma mpaka 3yrs? dziko silingalemere azibambo mukuvulila ana
Nde zimakhala bwanji, mpaka wa zaka zitatu, akakhale kundende moyowake onse
stupit man stupit idea
mmene atsikana akuphwekelamu?
Sad,angomva Kut Amakoma Ndi Maunda Chan?
Ameneyo angophedwa basi iyya
Shame..
Weeeeeeeeeeeeeeeeeee my malawi what are you turning into?
Into 53 years of independegwililira
Tsek wena
Sodom and Gomorrah
Very bad
kukhwima et mpaka wa 3 yrs its too much
Anthu amtima wawuchaponda ndi ambiri
I hope Malawi has the death penalty for animals like this!
alomwe alomwe!!!!!!!!!!