![Joyce Banda](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2015/10/Joyce-Banda-235x176.jpg)
Unyolo wa JB ulipo tsopano – atelo Apolisi
Patangotha masiku mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika atapempha kuti mtsogoleri opuma a Joyce Banda abwele, Apolisi nawo alengeza kuti akufuna kunjata mayi Banda. Malinga ndi chikalata chimene asayinila Bambo James Kadadzera amene ndi… ...