![Kasman](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/Muhmmad-Kasman-235x176.jpg)
Nzika ya ku Britain yabedwa ku Lilongwe
Apolisi munzinda wa Lilongwe atsimikiza kuti nzika ya m’dziko la Britain ya zaka 26 yabedwa ndi anthu osadziwika pomwe imachokera ku mapemphero Lolemba masana. Malingana ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu,… ...