The Midima senior resident magistrate has sentenced 25 year-old Malawian man identified as Amin Mailosi to 8 years imprisonment with hard labor for raping an 11 year-old child.
According to assistant public relations officer for Limbe police, Widson Nhlane, on 29 September 2015 the convict went to his garden where he enticed the victim and raped her.
“When her relatives heard of the incident, they went to Mailosi’s garden and took him to the police station,” said Nhlane.
In court, the beast asked the court to be lenient when passing judgement as he is a responsible person and he looks after children.
However, the magistrate said defilement is a serious offence which attracts a maximum sentence of life imprisonment but he sentenced the sex offender to eight years imprisonment to deter would be offenders.
The rapist hails from Kapsepse village, T/A Bvumbwe in Thyolo district.
Kugwilira ndikupha komwe chifukwa pamenepo mwina mwanayo wamupatsa matenda ine ndikuti zakazo zachepa kubeleka ndi kulera mwana ndi zinthu zowawa zedi
Kugwilira ndikupha komwe chifukwa pamenepo mwina mwanayo wamupatsa matenda ine ndikuti zakazo zachepa kubeleka ndi kulera mwana ndi zinthu zowawa zedi
RIP
Shame On U
mayi malawi needs prayers
Sizoona.
But gwaladi-raping case has died a natural death
Anthu amenewa afika ponyasa dziko muno koma ngati chili chiwanda chabwera udyo ndiithu,,kenako tizingopha stupit
Asa koma iwe!
Y these youngsters guys? Asiyeni pangani za aow a level yanu. Mukuwaopa kapena or kufunsira kukukuvutani?
Mwati 18yrs or 8 sindikukuvesan adimn rape charge
Why Eight yrs the judgement is very fair,Pamenepo amuonongela tsogolo mwanayo samapanga ndimwana wake bwanji?nwadays nkhani zogwilirazi zilipaliponse,my worry is nanga akavomeleza khalidwe la Mathanyulali how worse wil it be
Zachepa zaka
Zopusa basi kusaberekatu konseko. Ine agalu anthu ogwililira amandimwa magazi kwabasi. Achichepetsera zakazo
a form four guy will go to the university and finish his five years degree and his masters eeeeeish wastage of time neh
Asaaaa galu ameneyo msekereni. Chani mahule onsewa?
Nayeso osakanyenga hule bwanjiii?zopusa basi aseeeee
Majaji akumalawi alibe chilungamo wina waba chimanga zaka 10 wina wagwiririra zaka 8 mmm Jesus.
mwamuchepesera zaka ameneu
Eight years only?? Thats too lenient!
Akusiyana 14yrs! Enanso Ali Mabanjamu Ozdiwika Amasiyana 20yrs Kumene! KkkkkWa Cashgate 3yrs Komaaaaa!
Boma ndilopusa kwambiri.munthuyi alakwisa kumamanga zaka 8.akanadikila kaye kuti awone ngati mzimayi ali ndimimba.nanga akhapezeka kut ali ndi mimba mwana azasamale ndani?kenako muziti ana amasiye akuchuluka,mesa mukupangisa kut anawa achuluke ndiboma lomwelo?akulu akulu a zamalamulo ndi mbuzi za wanthu saganiza akafuna kugamula mulandu.mwamumanga azatuluka ndipo azagwilililanso mkupelekanso mimba ina.enawatu kugwiliraku sikufuna koma mfundo zoti awauze azimayiwa zinatalikila mwa iwo.mukanamufunsa kaye mzimayi ngat mamunayo akumufuna musanapange zomumanga.fuck kwa akulu akulu a zamalamulo big fuck
Simzimayi koma mwana wa zaka 11 wamva?
Yeah mesa paja tianato ndtimene tikukhala nayoto
Iiiiii ma guy nyere zimenezi zikumachokera kuti kodi?
Kodi mahule sawawona anthu amenewa akutichititsa manyazi azimangidwa zaka olo 40 ma hule alipo ambiri pali otchipa komanso odula ndiye azisankha malinga ndi mthumba mwawomo
vuto ndichan kodi?but do these men have sister’s too?i think i should start making artificial woman private part,you can make alot cash
Dziko ili sila chikhrstudi bible imati ochita rape azikwatila mkaziyo ndiye inu mukuzondotsa
Yacepa kwambili anali kufunika 25
Koma zaka 8 zachepa anthuwa akuzolowela kugwililila koma ma hule ali mbweeeee.
achepesa dzakazo coz mchitidwewu ukuchukila
Wadya ndithu Nanga akapeleka mimba mumutulutsa akasamale mimba ndimwana wake
25 naye ndi mwana zaka zikuthamanga inu masiku ano
Chtdwe Umeneu Ukuwnjeza Kwambr Mun Dzko Vuto Ndan Kma Anawa Kapna Ife Akul?
yap dat z gud let law take its course…..