Chakudya chavuta mu ndende za mdziko lino pomwe akaidi akungodya nyemba zokha kapena phala chifukwa cha kukwera kwa mitengo kwa zinthu m'dziko. Ndizachidziwikire kuti kudya kwa kundende kumakhala kosiyaniranatu ndi mmene anthu ena omwe sali… ...