Tikulemba anthu opuma pa ntchito kuti tibwezeretse mwambo mu boma – Chakwera
Pulezidenti wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati boma la mgwirizano wa Tonse likulembanso anthu opuma pa ntchito kuti athandizire kubweretsa mwambo pogwira ntchito za boma. Iwo ananena izi ku nyumba ya malamulo pomwe amayankha… ...