Minibus Malawi
Anthu oyenda maulendo osiyanasiyana pa Minibasi kuyambira lero ayamba kulipira mtengo okwelerapo kamba ka kukwera kwa mtengo wamafuta a galimoto m'dziko muno kuchokera lolemba. Kalata yomwe alemba eni Minibasiwa pasi pa bungwe lotchedwa Minbus Owners… ...