
Mighty Tigers yapata chipambano choyamba chiyambire league
Timu ya WakaWaka Mighty Tigers yapata ma point ake onse atatu oyamba itaswa PremierBet Dedza Dynamos 2-0 mu masewelo otola ma point mu 2025 TNM Super League omwe anachitikira pa bwalo la Kamuzu mu mzinda… ...