
Zipolowe zidabuka ku Zomba apolisi ataphulitsa utsi okhetsa misozi
Chipwirikiti chidabuka dzulo madzulo kwa Chikanda, Kazembe, Mpondabwino mu mzinda wa Zomba apolisi ataphulitsa utsi okhetsa misozi pambuyo padziwonesero zomwe adatsogolera ndi mkulu wa gulu la Malawi First a Bon Kalindo. Zipolowezi zidayamba pomwe anthu… ...