Palibe yemwe afe ndinjala – atelo a Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus McCarthy Chakwera watsimikizira mtundu wa a Malawi kuti palibe ngakhale munthu m’modzi yemwe amwalire chifukwa cha njala yomwe yafika posauzana m'madera ambiri m'dziko muno. A Chakwera amayankhula izi Lachitatu… ...