Boma lisamutsa msasa wa Dzaleka kuchoka ku Dowa kupita ku Chitipa
Boma lati lili ndi ganizo losamutsa msasa wa anthu othawa kwawo kuchoka ku Dowa kuti ukakhale m'boma la Chitipa. Izi lichita pofuna kuchepetsa kudzadzana kwa nzika za maiko enazi ku msasaku komanso pofuna kutsatira malamulo… ...