A Malawi ayembekezere kupitilira kukwera kwa mitengo ya zinthu, watero Katswiri pa zachuma
Pamene dziko la Malawi likupitilira kukumana ndi mavuto osiyanasiyana pankhani yokhudza zachuma, katswiri pa nkhani ya zachuma a Betchani Tchereni wawuza a Malawi kuti ayembekezere kuti pali kuthekera koti mitengo ya zinthu pa msika ipitilira… ...