A FAM mumakondela azungu – atelo a Malawi
‘Akakhala wakuda khungu ngati inu nomwe ndiye mumamuponya ku chipwete, akakhala mzungu koma si phuma lake.’ Uwu ndi uthenga umene a Malawi auza bungwe loona za mpira wa miyendo mu dziko lino la FAM pamene… ...