Zilikoliko 2025: Mutharika, Chikomeni awonetsa chidwi chodzaimanso
Pamene masiku akuthera kuchitseko kuti dziko lino lizachititse chisankho china mu 2025, Ras David Chikomeni Chirwa walengeza kuti adzapikisana nawo pomwe mtsogoleri wakale a Peter Mutharika ati anthu ambiri akuwapempha kuti adzaimeso. Nkhaniyi yayamba ndi… ...