Fisi anakana nsatsi: A Mutharika ati sakukhudzidwa pankhani ya simenti
Mtsogoleri wakale wadziko lino yemweso ndi mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha DPP a Peter Mutharika akanitsitsa mwamtu wagalu kuti akukhudzidwa pankhani ya simenti yomwe ilimkamwa mkamwa. Izi zikutsatira kutchulidwa kwa a Mutharika kuti ndiwo… ...