Kuli mfuwu ochuluka ku sukulu ya Ukachenjede ya Malawi pomwe bungwe lobwereketsa ngongole kwa ophunzira a m'ma sukulu a Ukachenjede alamura ena mwa ophunzira kumeneku kuti abwenze ma K175 000 omwe analowa kawiri. Sabata yatha,… ...
Apolisi ku Namwera m’boma la Mangochi amanga Abdullah Nandi wa zaka 38 kaamba kovulaza mnyamata wina Major Majid wa zaka 20 yemwe amamuganizira kuti anamubera m’munda mwake. Mneneri waapolisi ya ku Mangochi, Amina Tepani Daudi,… ...
Malawi Police in Mangochi district have arrested a 38-year-old Abdullah Nandi, in Namwera for allegedly injuring a 20-year-old suspected criminal, Major Majid from Traditional Authority Bwananyambi in the district. Confirming the development, Mangochi Police Station… ...
Two men from Mtandire Township in Lilongwe, are in custody at Lingadzi Police Station for allegedly raping a 14-year-old mentally challenged girl. The suspects are Charles Ngalawesa, from Makola village, Traditional Authority Chigalu in Blantyre… ...