M’modzi mwa akatswiri ochita zisudzo mdziko muno Andrea Thonyiwa amene amadziwika ndi dzina loti Mr Jokes, wapepesa kwaotsatira chipani chotsutsa cha DPP kaamba ka kanema yemwe anatulutsa oselewura momwe amayankhulira a Peter Mutharika. Mukanema yemwe… ...
Mponda matiki Thomson Mpinganjira yemwe wagamulidwa kukaseweza jele kwazaka zisanu ndi zinayi (9) wati sakukhututsidwa ndichigamulochi ndipo akuti akamang'ala kubwalo Supreme. A Mpinganjira omwe anapezeka olakwa pa mlandu ofuna kunyengelera oweruza milandu kuti akhotetse chigamulo… ...
Ngakhale phwando lamaimbidwe la Sand Music Festival latha, koma anthu akukambilanabe m’mene zinthu zina zayendera makamaka nkhani ya oyimba wa m’dziko la South Africa, Makhadzi, yemwe wasiya anthu akugundana mitu pamavalidwe ake. Makhadzi yemwe dzina… ...
Malawi Broadcasting Corporation (MBC) journalist Allan Phetembe has died  in a road accident in Neno district today. According to MBC Director General George Kasakula, Phetembe together with another journalist from MBC, one from Radio Maria… ...
The country's Department of Climate Change and Meteorological Services has predicted that most parts of Malawi will experience good rains in 2021/2022 rainfall season which begins this coming October. This is according to the Director… ...