A Malondera Aphungu a nyumba ya malamulo mdziko muno apempha boma kuti lilingalire zowagulira ma khotholo kuti asamanyowe pomwe akukalowa mnyumbayi kuchokera pa malo osungira ma galimoto. Izi ndimalingana ndi phungu wadera lakummwera chakummawa kwa… ...
Zina ukamva kamba anga mwala. apolisi ku Zomba akusakasaka mbava yomwe yaba mfuti, zipolopolo khumi komaso ma foni a m ’manja awiri mu ofesi ya apolisi. Malipoti akusonyeza kuti nkhaniyi yomwe yadulitsa mitu yazizwa, yachitika… ...
M’modzi mwa anthu omwe akhala akutsogolera a Malawi ku ziwonetsero zomwe zakhala zikuchitika mdziko muno posachedwapa, a Bon Kalindo, alengeza kuti ayimitsa kaye ziwonetsero zonse zomwe anakonza kuti zichitike. A Kalindo omwe amadziwika ndi dzina… ...
Mpondamatiki Thom Mpinganjira tsopano akupuma mpweya wabwino bwalo la milandu la apilu litalamula kuti atuluke ku ndende pa belo. A Mpinganjira analamulidwa kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu ndi zinayi (9) kaamba kowaganizira kuti ankafuna… ...