Days after reports emerged that former Malawi president Joyce Banda was the chief architect of the infamous Cashgate scandal, a television station linked to her has started airing.
The television station which comes after her Ufulu radio station is also called by the same name of Ufulu and started broadcasting on Wednesday evening.
A message that was scrolling over indicated that the television was still in its initial stages and had not yet started broadcasting full programmes.
As we went to print, the television was playing music videos of both local and international artists.
Ufulu television is set to join a list of other television stations that include Bakili Muluzi owned Joy television, state broadcaster MBC, Lilongwe based Luso television among other television stations.
Kodi anthu mumavutikiranji ndi kutukwana onbehalf of politicians, anthu wa amadyera limodzi, JB ndi Peter yo akudziwana, mungodwala nazo ma BP za zii, pangani zoti zikuthandizeni inu ndi ma families anu
Some tyms munthu akamalephera amachulutsa zonena. Musiyeni JB. inu osanena za chibudzi agula madala anuwa bwanji? Anthu tikuvutika wina atikumakagula chimbudzi cha ma million ambiri mbiri. Pali nzeru apa? o.
Mayi wanyeru uyu omsansokoneza maganizo. Musiyeni apume mwa mtendele
#most_welcum_ufulu_tv
Thats how to fight evil replace it with Good way to go Mama…….
Sizikugwilizana ndi jb mind u
انا عـرفت مين زار بروفايلي اعرف أنـت كمـان مين زار بـروفايلك بالـوقت والتاريخ و معرفة الوقت الذي يدخل و يخرج به اصـدقائك . شاهد الشرح ^_^
تأكد من تعليقات الزوار قبل اى شئ
من هنا ==> http://arnewst.blogspot.com/5 ↓
mukutukwanana why? there isn’t need 2do that after all its part of development in our country. all of us we are going 2benefit as a nation. don’t bring politics ln every issues on fb. ndale ndi nkhani iyi zili kutaliiiiii. Dpp woyeeeeeee
akulu enanu talembani zomveka,nanga alipo president wotchedwa mbakili and bigu mu malawi muno?,nanunso makape kungolemba chizungu cha bodza apa,asah!,go back 2 sch & learn first,mbuli zachabechabe, ati “pple himselves” nde chani?
Zapo kha!!!
Write about peter
A 24 nanuso mukumasuta ndi kumwa eti
My wish is apeze ma best prisenters and Good programes,,the should follow suite of Times Tv. BRIND PIPO LYK #LODZI SONKHO
tionere zimenezi
nc
nc
Ufulu ufulu chiani, umbavao kupusa
zaziiiii…… vuto atsogoleri akumalawi akangoba tindalama amangothamangila kutsegula tima Radio station tima TV station, kod palibe zina zot mungatsegule, cholinga muzibakilidwa nd nkhani zonyansa zomwe kkkkkkkk kma ku Nyansalande
on the very first day testing its transmission, i enjoyed it,like wise Matindi tv,Beta as well as Timveni,to me what i want is maximum entertainment in my house,period.
Poor mindded you 24pipo bola UTV than yaboma kkkkkk
Amalawi tiyeni tisiye sanje ndi kaduka sizingatithandize
That’s good development timafuna zimenezi kaya ndiyandani we don’t mind better we have many channels to choose we can’t afford DSTV so fake Journalists you have guffed kupanda JB kulamura bwezi tikuonera only TVM ma licence apeleka Amayi
wow,,wat a TV station,,quality,,nice pictures,,Ufulu ndi deal.
May ando ana kuyamikilan pamaliro amandela
Ufulu tv woyeee proud of you JB
Malawi ndinchoncho Sanje Basi
JB ndiwa Ndalama kale mumangovutika naye
Ali pheee ku RSA timakumana amatithandizatso kuno
Ngati mukumfuna mundipeze ine
JB. HOYEEEE
mayi wakubayo akufunidwa kuno,analakwadi akuthawa chani, anaphunzisa azimayi kuba ameneyo.
nanga akuba ali muno mukungowaonawa bwanji? talimbanani ndi zooneka ndi maso. anthu akuvutika kucipatala, ku admarc.
palibe vuto its a development to this country ngati zikukuwawa zako zimenezo Joyce banda Ali ndi ndalama osati za cash gate usiru eti
Ndata /GOLIATI tv kkkkkk
Enough! & you’re making her popular than your president himself
Ok nkhani yabwino mwina nkupuma kuwonela uyu gay
But malawi is not poor nation but people him selves are poor
pple himself yemweyo hahahaaaa
Tazilembani chichewa paja English is expensive nanga MPAKA himselves are ndiye chizungu chanji ?
kkkkk #mada inenso ndi madabwatu kt pple himself ? mwina si ENGLISH koma ENDLISH
Mpaka pple himself kkkkkk
koma iwe Mw 24 indisamale dairy JB JB ok timakuonatu
What A Prosperous Mama Malawi Proud Of U,
Imeneyi ndiimene ndiziwonera dairly,osati mbc ya mr ibuh.
Apereke umboni wake naye otsati mutseke pakamwa ayi mbakili zache zinantha bigu anachita kumwalira khani ndiya JB Basi naye awonekere kokhoti basi
So tv ndi cashgate zikugwirizana bwa? Ndekuti galaxy nayo inali ya cashgate
Welcome ufulu tv
If really she was involved in the cashgate issues why can’t you take over some of her investments
Police clearance
Udadya nao zacashpate et bwanji ukukwiya usakwiye munthu!
Amayi tapangani zomwezo ,pa DSTV ndingaipezepati plz
thumbs up chi mbc shupit station alwayz pitala
Yaa good Development! !!
Bakili anaba Bingu anaba Joyce Banda anaba Peter nde ndi ameneyu so what ? to hell musatinyase.
A imwe mwayowoya unenesko mwe,This peter started when he was minster of education until now
Mmm i think the one who tipe this shit is anmol is battar to shat upp ur mouth if u dont have some thing to say fuck u
Big fuk u
employment opportunities
Olo mutamapanda kumvera/ kuonera, mind u Malawi ili ndi anthu ma million ambiri oti azionera…inu muzionera mutharika broadcasting station yo
ife sitizionerabe jb wa manyi
So what??????
Viva JB- za chamba eti!! Aimanso 2019
Emloyement opportunities
Lumbadzi police station ikumudikira ameneyu akuchedwa.
So what??????????????
So what???????????????
Mwasowa nkhani yoti mulembe,u don’t know work go back school mukayambile std 4.Mpite limodzi ndi bwana wanu akayambe std 3d.
Joyce Banda ndi dilu deile tingowelenga khani zake pa fb
Kodi ngati ndi Mbava ndiye pakuvuta pati kuti mwamange mayiwa
Inenso tu kudabwa nawo monse adayambira kukuwa muja …
As if JB yoo ali ku mwamba osakamutenga bwanji
kkkkkkkk anthuwa bodza basi
Nkhawa Njee!
What is the name of tv want to tune on
UFULU TV
818 on Go tv
munya simunati # team jb
Hahahahahahahahahahahahahaha sindine wandale musanditseketse anthuni.
Ndisanve kuti wina akufuna atseketse Tv station ngati anthu alembedwawo awapezera zochita.
Ndalama za cashgate sizonyadila itsekedwa posachedwa tikuonelani & ine sindingakhale busy kumaonela ufulu TV kapena Ku Vela ufulu radio.
Zinyere!
hahahaha inu ndiambuli inu
Ndiye ukasiya iwe ife tikwiye? Mbuli ya munthu
ukuchedwa mmene ibebera ufulu
Nanga Siamakutuma Agogo Akowa Kuti Udzigeya Matuvi Akowa. Ife Tidziwonela, Bawoonelani Peter Muthalika Tv Yanuyo.
Kkkkkkkkkkkkk Bigman Ndi Banjalawo Kkkkkkk Mpakana 2019 Wooooooo!
Kkkk mchere uwo mchere uwo ulemu wanu bwana asafuna azilume kunsana.
Nazooooo
Kkkkkkkkkkk Abiti Getrud Ndi Che Pitala Kkk
Koma amaa amaa maa ,amaa inuyo mmmh ndinu dolo amene zamuwawayo agonane ndi mkhumba
koma Malawi 24 ulindivuto
,n m.,,. …,.,,
Kodi mukapanda kulemba za Jb ndiye kuti tinkhani tanu anthu sawerenga?
Bwerani mayi takusowani
so what? fodya eti
Clear pictures on Ufulu tv
you Malawi 24 u mean u dnt have other stories to write? daily za JB mxiew we r tired with these stories mwamva!!!!! shitt
Try this one: http://malawi24.com/2016/01/07/patients-keep-sleeping-on-the-floor-at-qech-while-mutharika-spends-millions-on-his-toilet/
kkjkkkkjkkkj koma ngoma
BASI
zikutinyasa heavy!!!!! iyaaaa
Hahahah,,channel 818 on Go tv,,thus Utv,,ufulu Television kkkkkk
Zaziiii we need our money!
pse kindly go to ndata, and galaxy tv for your money.
Muli bho amayi
Ka tv kalibwino aka.
Koma ndiye mwasowatu zolemba palinso nkhani apa ndichifukwa malemu Bingu ankati mukasowa cholemba muzingojambula ng’ombe basi!!!!!!!!!!!! Mumafuna azungu ndiye atsegule TV ku Malawi kunooooo!!!!!
Tsegula yako naweso , apo ayi ingofani
Ndmafuna ndigule DSTV komano bansi
Tiitseka pompano siikafika patali
Wanya basi
Wanya
itsekedwedi
Ukukamba za TV ndiye nkhani ya cashgate ikubwerapo bwanji? Kusowa zolemba eti?
Ufulu woye!
Yea. Bravo Jb, You Did Not Legalise Gay
Ifetu ndizomwe tikufuna kuti ma station achuluke mudziko
Ufulu Tv Bola Pamenepo
Koma ndiye yili nyatwa…we are enjoying it
Ili Pa MBDN DECODER?
CHANNEL CHAJI?
Yayamba Liti
Angulube
Go tv,,channel 818
Ohk
ufulu tv yomwe kuti wawa mwina tipume kumangoona mr IBU opanda manoyu kkkkk
Noma yomweyo..
Asernal woyeeee
Kanthu ako! Malawi woyeeeeeeee
she has a t.v.
UFULU TV WOYEEE!!
hahahaha
Kkkkkk Malawi
Ufulu Tv.
What is pleasing is that these new television stations are coming up with High Definition equipment as a result the quality of pictures is so good!