Members of Malawi’s People’s Land Organisation (PLO) and Citizen for Protection of Mulanje Mountain (CPM) based in Mulanje and Thyolo have denied reports that the two districts will become independent if government fails to resolve land disputes in the district.
The development comes after the chairperson of PLO, Mr. Vincent Wandale, told reporters last week that the two organisations, PLO and CPM, have given government 17 days ultimatum to resolve the land disagreement failing which the two districts will form an independent state.
Speaking at a press conference on Friday, public relations officer for CPM, Bon Kalindo said Wandale’s claims that the two districts will become independent were his personal opinion and not the views of the organisations.
Kalindo wondered why Wandale delivered that speech when the groups on October 15 met the President Peter Mutharika and discussed the way forward on the matter.
“We met here in Thyolo to clear what Mr Wandale has said. He has said Thyolo and Mulanje mountain are to become independent and be called United states of Thyolo and Mulanje if the government and the president fails to resolve the dispute, that is not true.
“He should not pretend to have said this on behalf of people in these two location, I think he has said this on a personal basis,” said Kalindo. He added that if anything will happen within the said 17 days, Wandale will be responsible for that and not PLO or CPM.
However, Wandale called the accusations senseless saying what he said is what PLO and its members agreed on 26 November at a meeting. He said he is there to fight for people’s land and says no one can threaten him.
vuto la alhomwe kusaphunzira. akuganiza tiyi wawoyo azigula ndani akakhla independent? usavage basi
We are a PATHETIC NATION …….we are very stupid……ka dziko kake komweka kakutivuta kuyendetsa nde wina kumakambaa zopusa….its better we call azungu azatilamulileso…..democracy tainvetsa molakwika n sitikudziwa kuti tikutani….our foolish leaders stop doing things everything mu ndale
Uchindere wakufikapo…
Iweyo ungadandaule,wabva Chikopah?
Or mutakhala independent ndi ndani angakudandauleni?
Hedeeee dziko palokha misala eti
Musaope malo ndi anu si azungu!
kampeni ya winiko kuti awine inali imeneyi ndiye zachita bwino ndithu mukathyola tea wanuyo zisinjani nkuyanika kenako mumukazinge muchiwaya mukatero mupeze ma buyer anu muone mmene mufiirere maso kodi mumaona ngati azungu angakusireni factory yaulere eti muziganiza mukafuna kuyankhula MUTOMVA A LOMWE INU
Tapitani uko inu tamakachekani matabwa kuchikangawako…… Nkhani ilipano siimeneyo uwerebgeso komano vuto siiwe ima kaye ndikulembere muchitumbuka kuti umvetse wapulika mbwenu mbwenu
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk koma yah mmmmmmmmmmh eishhhhhhhhhhh
Kkkkkkk! Paja mlomwe weniweni amayenda ndi mpeni kulikonse akupita. Zibayanani komweko ndi kukula mitima kwanuko.
Paja ambwenu mbwenu sumutha kumvetsa nkhani eti…… Nanga nkhani ikukambidwa apapa ndizimene ukunenazo zugwirizana chani…..? Wangosiya kuweta ng’ombe dzulo lomweli eti….? Nkana sukudziwa
Kagwere uko nawenso iwe. Wakhuta nandolo eti. Si za personal izi, wamva?
Aloleni apange zomwe akufuna mwina makopon mkutupa kkkk
Afiti awa asatibowe mwamva? Malo si a mwini wake Mulungu kodi? Nonse mudzafa, malo mudzawasiya awa. Alipo munthu amene anabadwa ndi malo?
if it was mpoto it coments wud be atumbuka inu sht pple
ADAKAPANGA ZIMENEZO ATUMBUKA. ZOYAKHULA ZIKADAKHALA BWE! E
Thanks Aristobulus Chipie Sambani for your support on my comment.
KENDO. izi ndiye zachamba we ar all malawians choziimira iwo pawokha ndi chiyani?
President wa alomwe Mr Winiko B Kalindo anatsutsa kale zimenezi
Amalawi chenjelani ndi ma LUANDAN ndi ma CONGOLISE. Ali mmomuno ali kaliki liki kufuna kuzesa chipolowe ndicholinga choti Kuno ku Malawi kukhale nkhondo.
Which group r u sain adimin? Cuz im here in thyolo.mbolo yako admn.
Apa mwaonetsa ulomwe wanu ndi uchitsilu onse, chotukwanila ndi chani zinthu zoti dzulo awandale amalankhula pa times radio masana, bwanji osafufuza kaye musanalembe zanuzo ?
inenso sndkuonapo chotukwanira apa,,eeeeeish
baba wandale anzanu zawakanika zogawana boma
Aime Atengenso Ndi Peter Emwei Akhale Wao
Malawi is small country
kkkkk-kiii!! who will b mr.president sir?
Kkkkkkk ku thyolo & Mulanje samalima chimanga::::aloleni akhale paokha azingomwa tea Kkkkkkk
Munangodutsa munseu,simukuidziwa Thyolo ndi mulanje,,,chilichonse timalima ku Thyolo n mulanje,
Sakukudziwanso ku mulanje uyu
Chilichonse chakumunda chiliko, mwina mumangomvera kwa ena man.
Mukudziwa anthu aku mpoto amabwerera pa Blantyre nde mkhulukiren sakudziwa kwinako
Aah Mulungu Wayankha My Prayer Peter Mutharika Akhale Kwanukotu
Iwenso ndi Mtumbuka eti zidya Fodya yemwe umalimayo
inuyonso muzimwa tea wamakaka osakaniza ndi nandolo akwa Bondo kumbiya makaula namazoma supuni mimosa limbuli nkuta nyalinga
Ambwenu mbwenu palibeso chomwe amadziwa anthu oti akulira kucheka matabwa kuchikangawa town ya BT angoidziwa kumene asiyeni angochedwetsani
Adazolowera ku lisha ng’ombe ndiye paja phwitsi ya chiweto chimene chija chimapeperetsatu…kikikikiki mix yao ija yochita chiwere ndichiwetocho mutu ungagwire
Agalu/tchewe mungaime panokha kkkk tea omwera nthochi? kkkkk vindele
Mulanje en thyolo belongs to Malawi,those claims were made by a confused leader,who lost direction, PLO en CPM have clear objectives, to speak fo the voiceless
http://theyouthjob.com/?ref=194304
If they want to be independent,let them be independent but the land shall remain the property of the person that is using and owning the land despite the race, nationality or religion.