Apolisi awiri awachotsa ntchito ku Thyolo
Nthambi ya apolisi dziko muno yachotsa ntchito apolisi awiri amene amagwira ntchito m'boma la Thyolo chifukwa cha kulephera kusunga mwambo komaso kujomba ku ntchito mopanda chilolezo. Mu kalata yomwe wasainira ndi wachiwiri kwa mkulu wayang'anira… ...