Wanjatidwa kamba kogwililira ana atatu a zaka zinayi
Mnyamata wina opanda dambisi wazaka 18 wavekedwa zibangiri ndikusungidwa mkambolimboli ndi apolisi m'boma la Thyolo kaamba komuganizira kuti adagwililira ana akazi atatu a zaka zinayi zakubadwa.. Nkhani yonse ikuti nyamatayu yemwe dzina lake ndi Milwad… ...