Khoti lati ligamura Mlandu wa Kalindo mawa
Yemwe akumva Mlandu wa Bon Kalindo, Rodrick Michongwe, wati apereka chigamulo chake pa mlanduwu mawa nthawi ya 9 koloko m’mawa. Oyimira a Kalindo pa mlanduwu a Khwima Mchizi anapempha bwaloli kuti a Kalindo apatsidwe belo… ...