Kodi munthu nkukhala yekha? Driemo wazula wake pa Zambia
Ba neba kumatipatsa ulemu ndife amuna anu: Oyimba yemwe watekesa pa Malawi Driemo, watutumutsa gulu pomwe zikumveka kuti wazula wake pa Zambia. Nkhaniyi yadziwika lachinayi pa 24 August pomwe oyimbayu yemwe watenga chikoka cha anthu… ...