Wagwa mpesa; chinkulirano chabuka ku SDA yakum’mwera
Maranatha! chikondi cha pa abale chipitililebe: mpungwepungwe wabuka mumpingo wa Seventh Day Adventist pomwe akuluakulu a mchigawo chakumwera alavula nthambi ya Bangwe kuti simbaliso imodzi ya mpingowu ponena kuti ikuchita kusaweruzika. Izi ndi malingana ndi… ...