
Alibe moto Chakwera, anthu atopa naye – atelo a Katswiri a kafukufuku
Chikomekome chamkuyu... Ngati alipo anthu akugomelabe utsogoleri wa Chakwera ndiye ndi kutheka ndi a pa banja pawo ndi nduna zawe zokha basi. Mwina ndi a Yufi owelegeka. Chifukwa kafukufuku waonetsa kuti pa a Malawi handede… ...