Bambo wina wa zaka makumi atatu kudza mphambu zisanu ndi imodzi (36) ali m’manja mwa Apolisi a mu boma la Lilongwe atapha mkazi wake.
Malinga ndi Apolisi, bamboyu ndi a Major Wilson ochokera mu boma la Mulanje.
Apolisi ati Bambo Wilson anakhala pa banja ndi mkazi wawo kwa zaka khumi ndi zisanu (15).
Iwo ati anauza Apolisi kuti masiku atsopano anakhala akumva mphekesela yoti mkazi wawo anali kuyenda ndi amuna ena.
Ndipo tsiku lina anapita pa okala ya banja lawo pamene anasiya akazi awo. Atafika kumeneko anapeza mkulu wina akuzagula malonda. Iwo ati anadabwa ndi machezedwe a awiriwo ndipo anakayikila kuti mkuluyo anali m’modzi mwa oyenda ndi akazi awo.
Iwo anathamangitsa mkuluyo ndipo atapita kunyumba anayamba kukangana ndi akazi awo.
Ati iwo kenako anatenga Bango ndi kuwamenya nalo ndipo iwo anathawila kubalaza kumene anakafela.
Koma a zachipatala ati mayiyu anamwalira kamba kovulazidwa m’mutu ndinso kutaya magazi ochuluka.
Bambo Wilson akuyembekezeleka kupita ku Khoti.
Ndikumva kuti watuluka, Is it true?
Zavuta galu wakodzela thumba la alendo.
mbuzi
Ndimuthu wolimbantima yekha amangozisiya
mangowo ndawakhumbira
ndinawadya pakanthawi
My god bless malawi Eish
Kupha Mkazi Chifukwa Chasanje Sibwino Ayi.Ndibwino Kumusiya Mkaziyo,akazi Onsewa Man Ndiye Mupangitsa Kuti Ana Akhale Pamavuto Tsopano Chifukwa Chazibwana Zanu.
Walakwa kumupha bola mukanamusiya banja mkazi wachisembwereyo
Ooman di best gift God Eva gave man…nuh abuse dem ngati zavuta straight divorce affi gwaan
Zatero kodi ati…. Nkhani yomvetsa chisoni kwambiri… I think Pena pake akazi azitha kudziziwa kuti ali PA banja… Kotero akuyenera kumupanga zinthu zoti zisasemphane ndi zomwe mwamuna akufuna
akaz mwajayra kwambiri munyamuwona
Mmmmmmh
Anangomumenya ndi bango nanga mpeni uli ndi magaziwu
2bad
Amazfra Akaz, Kut Azmenyesa Paliponse.
better end of love,accept killed no
Koma dziko latha.mkazi kuphedwa ndimamuna wake anthu inu kumayamikira mulungu akukhululukileni njira yabwino kumusiya mkaziwo ali moyo iwe ukwatira nayenso akwatiwa moyo wanonse kumapitilira.akazi onsewa akusowa amuna nzeru yofunsira inathera pa iyeyu?uhulewo amachita ndi thupi lake.bambo uyu aphedwe mwinanso uhule amachita potopa ndinkhanza zachigawengachi
y Malawian men like to do this.Y if you see that she doing wrong things just throw him away then find another onather one there is a lot of ladies in Malawi please stop this
Olakwa ndi mkaziyo koma mamunayo walakwitsa kuphako.
Nanga kumenya ndibango inu mkukajambula mpeni wamagazi.nge kuputsako.bwanji osagambulapo bango
wachita bwino kumupha azazolowela
Akazi mukadafa akapekanso wina timuotcha asamativute timaononga ndalama kut azifika pomawasilira amuna enawo.
zoipa izo, malamulo agwila ntchito.
Chikondi ndi chovuta R.I,P
Zovuta
kupepela 😀
Mkazi anali wabwino kma osamva za wina nayenso mwamuna walakwa kupha bola anakamusiya
Kuchidapa bwanji ankaz Ali palipose akusowa amuna asaaaaa koma nanu ankaz musiye ma social media ndipo mmapezela zolakwika mpaka akukuphani
bambo wina wodziwika ndi dzina loti Bilton Wapha Mkadzi Wake Ku Mangochi, Namwera Kwa Mwawa Pa Chifukwa Chomwe Sichikuziwika Bwino, Bamboyu Ndi Wazaka 58 Ndi Mayiyo Ndi Wazaka 51, Pakadali Pano Ali Mmanja Mwa Apolisi Kaya Malawi24 Inali Kuti?
Koma iwe ulindiumboni?
kkkk ndi bodza eti?
ife zbwenz and banja ai zachan tmangoganyula wadya balalikan kuopa zngt zmenez mabanja ali akale pano maganyu basi.
The headline and picture itself totally parallel I can’t even bother to open that damn link wagwa nayo admin!!!
Munthu sumachitira nsanje chinthu chilii chako kale. Kuphako walakwisa koma mau oti sanje si olondora.
some women r like internet viruses,they enter into your life,edit your mind,scan your pockets,download their problems & delete your smile
Nkhuku yoweta samagula pa nsika.Zomangotolanapozi kaya,lero ndinu mwayamba kuchuchitsa mwazi.Chitsilu kumakachitula kwa mwini wake,chimakhala mpokomela kwa mwiniyo.
Sitikulemekeza Moyo,akazi atha? Vuto losadziwa kufunsira ndi limeneli,wakundende basitu supadzapaonanso,ambuye akuyendere munthawi yakusautsika kwako!
Kkkkkkk,sazapaonanso eti?koma yaaa.
Mmmmmm shame
komadi pano zanyanya ndithu Amuna kutopa uku koma tipeza njila INA yowa phela kupatula yomenyayi ndi #madamu-kesi akazi aonjeza ndithu ndi fiti ziphedwe basi tizigwilitsa ntchito poison kuti azikafela kwawo tisamamangidwe Amuna ambili pano pakhomo kumapezeka ana 5 popandapo nmodzi wako akaganyule uko akaona kuti nmimba mwatentha basi ndi we bae bae bae ndili after iwe lelo lose lino ndeaku bwinditse mowilikiza mawa ndilinalo akuuze Kukhala Ngati ndili ndi mimba iwe nkuganizila ndi game nmomwe unachitila sukana umangoti tisamala eni ana Ali pheeee kwawo aphedwe ife tinasiya zosilila kukwatila or chibwezi zikavuta timakagula VIP Ku bwandilo kapena tchezi ntemba no mathathixo
Hmmmm,maganizo a chabe
Mmmmmm last days
mayazi mumati size akazi inu kumafatsa osati uku mwendo mwaukweza uku mwaukweza eeeeeeeee
wamupha uzichonda bwanj? timanena mkazi sing’oma.nkutukumve
azibambo tikulera ana anthu ena mmanyumbamu ife kumaona ngati athu ndithu
Kkkk eish man
Palibe cholakwika pamenepo wapha mbali imodzi yathupi lake baibolo litero mkazi ndi mamuna ndi thupi limodzi ndiye palibe chomangira muthuyo atuluke basi bola kumanga Chaponda anaba ndalama zathu
sizikugwilizana, kambani za izo
Nsima Munthu Umatha Kuitanira Kwa Mzako”BWERANI TIDYE NSIMA?”nanga Kodi Ndindani Adaitanirapo Chisebwere”BWERANI MUZAGONANE NDI WACHIKONDI WANGA?”nsanje Imapha Nazi Tikumvazi,maliseche Asiyana Ndi Chokudya,posewera Ine Kumva Kt Wina Akulakalaka Kusewera Ndimusowesa.Uyo Walakwa Kupha Bebi Malo Moti Akadathana Ndi Uyo Amamuganizirayo.Kaya
ZAboza izii guyz
Apha Mkazi Atamummenya Ndi Bambo,umenewu Ungakhale Mutu Wa Nkhani?
BAMBO APHA MKAZI WAKE.
mwaona bwanji pamenepo. zisiru za atolakhani a J.C.E certificate.Learn To Compose Headline.
Life Prison
“mmmmmmm” nkhani zina ndizovuta kuti uzimvetse, nkhani ya zibwenzi m’banja kunena moona akuchulukira ndi azibambo. Ambuye atithandize ndithu.
Uyu wapha mkazi wake, mmmmm Ambuye achite naye. Mzimu wake uwuse mu mtendere “rip”
Boma lichitepo kanthu kwa anthu ngati awa.
Shame mpaka kupha mkazi khani yake yomweyi
Choka Iwe Ukuziwa Chikondi?Kodi Ukuyesa Malise Amkazi Ndi Nsima Yoti Ukhoza Kunena Kalibu?
Ndiye mpakana kupha mkazi ?????
And #Alice_Port_Mwentete kea orata. you are so beautiful.
Malawi24 dzukani plz
TIMVE ZABANGO KAPENA TIKHULUPILIRE ZA MPENI TIKUUWONAWU?ndiye kuti nkhani ndiyabodza.
Mpeni Ndi Simble Ya Imfa Doesnt Mean Akadajambula Bango.Roadsign Akajambula Hospital Mean Hospital Ili Pa Msewu.?Tamaganizani Ngati Anthu.
It’s a true story, but nobody knows kut anammenya ndi chiyan, since zinachitika usiku i knw them all.
kkkk azimai awonjeza uhule alipabanja koma zibwenzi
Mukuti wapha mkazi wake ndi bango picture mukuikapo mpeni muthaunza chiyani mukuuza mwana
eeesh osangomusiya bwanj
Wachita bwino kumupha azimayi panopa awonjeza zibwezi ndi zima facebook izi, uzapeza mzimayi usiku wapakati ali pa line funso limakhala loti akucheza ndindani 1 am
Mmmm!
Mwana Ukuti Ndiwakoyo,Aise Uiwale Mwini Wake Ndi Friend Wanga Wamva..!..!
Aaaaa osangomusiya bwanji? Akazanuwo munawamba ndinu? Mutamusiya simungapeze wina?
Ife tikudandaula kuti ngozi zapa nseu zachaluka iweso ndikukaphaso mkazi wako ndi stick magic yako aaa nayeso aphedwe basi kuti zithu ziyende boh
Ife tikudandaula kuti ngozi zapa nseu zachaluka iweso ndikukaphaso mkazi wako ndi stick magic yako aaa nayeso aphedwe basi kuti zithu ziyende boh
KKKKKKK NANGA MPENIWO?
koma znaz abale
Anali okhwima uyu #meja_willison wa kwa mgona
nde bwanji mwajambula mpeni? Mesa mukuti amamumenya ndi bango
zaufiti basi…bango lingaphe munthu?
Bango limapha ng’ona nde iwe ukunena munthu?