![Michael Bizwick Usi](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/Manganya-235x176.jpg)
A chidodo pantchito m’boma achotsedwe – Usi
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Micheal Usi ati mzosabisa kuti ogwira ntchito ena m'boma akugwira monyentchera kotero mkoyenera kuwachotsa ntchito kuti dziko lidziyenda. Poyankhula lamulungu m'mudzi mwa a Golden m'boma la Mulanje, a… ...