The court case against Malawi’s popular street-performer, Joe Gwaladi, in which he is accused of raping a 14 year-old girl will resume tomorrow at Phalombe First Grade Magistrate Court.
Gwaladi was arrested by Phalombe Police in May last year on suspicion that he defiled a 14 year-old girl. The Tumbocid hit maker hired lawyer Chancy Gondwe and he was released on court bail. He was ordered to pay a bail bond of K100,000 by first grade magistrate Damson Banda.
Phalombe Police Spokesperson, Augustus Nkhwazi, confirmed to the media last week that the case will be back in court on January 19.
However, the publicist did not explain why the case is dragging saying it is being handled by state prosecutors.
The “Ndikanadziwa sindinakapanga” star, denied the charges of defilement levelled against him.
Oimba mukamapanga ubwenzi ndi wana muzionetsetsa fwa ndinu anthu amodzi amene mumatsatidwa kwambiri. Komanso a gwaladi mwanyanya kuimba zolaula mpake ake sakukaika kuti munagwiririra
Gwaradi aribe problem mwana wazaka 14 ndiwamkuru akudziwa chomwe akuchita ANAGWIRIZANA
umaitha joe but zinkakoma bwana gwa?
malo mothana ndinjalayo apa..boma zamasikwano..gwalad amalakwa
Koma magalasi mukamavala kumafunsa ma neba kuti ndikuoneka bwanji?
Zinatha they are free usova atume zina akufufudzira ehede ukuchedwa
Kkkkk zavuta
pliez leave gwaladi alone
Abale’ Kodi ati Gwaladi atangoilowesa mtsikanayu amalilira kuti asachotse? Kkkkkk! Mwana amatero? Ifetu ATcheya anatiuza kuti Mwana wa mkazi akangomera mabere pa mtima basi wakwana ameneyo! Kkkkkk mmasuleni munthu according to Atcheya Theorem!!!
Koma Joe akut ndi mutu okha omwe unangosumira kumaloko koma boma likumusaka nanga adakalowetsa yose gwaladi bwezi atamutapa kholingo
Koma Joe akut ndi mutu okha omwe unangosumira kumaloko koma boma likumusaka nanga adakalowetsa yose gwaladi bwezi atamutapa kholingo
Ndiye yatha bwanji
Serious
Chikondi ndi magazi
Chikondi ndi magazi
d@ ma favouite rapper guyz musamumange
d@ ma favouite rapper guyz musamumange
mleken mphawi nzathu
Uwu nde usilu mukufuna kusautsa munthu ndi nkhani yogula maliseche mesa iye amadya ndalama yake, Kodi nanu aboma mukulephera kuzenga mlandu aCASHGATE, okuba Subsidy tools , NDUNA zogwirira zija zafodya basi iZAPSATU COURT kumalawi kuno
koma akhwaka nyuwanho tamusyen mfana wakumuz kwathuyo,It means tzgonana amuna okhaokha akaz tsamagonenawo???? mundyankhe ndsayambe kukumba munsewu!!!!
tiyeni tizaganiza amalawi bwanji mukuwasiya amuna akugonana okhaoka plz mutayeni Gwaladi alibe mulandu
Boma LA Malawi LA manyi akulimbana ndi gwaladi akanakhala kuti ndiolemera atazibisa kale bola lamtundu wanji lolimbana ndi amphawi
Boma LA Malawi LA manyi akulimbana ndi gwaladi akanakhala kuti ndiolemera atazibisa kale bola lamtundu wanji lolimbana ndi amphawi
Macourt akusowa milandu yoweruza?Akulimbana nza zii munyu nkhabe.
Macourt akusowa milandu yoweruza?Akulimbana nza zii munyu nkhabe.
Gwalad wakongola nd injen yomwe
Ruth Ayandah, akuti anagwililira mtsikana
momwe amalowetsa kwamanayo imawawa or amava bwino ngati amava kuwawa agwaladi asakane anagwiririla ngati amava bwino nanga chomangilaso ndichani poti amafilana boo?
Watchuka ngat xazamwalira
kkkkkk views
kkkkkk views
Komatu Joe Adakamba Kale Kuti Udangolowa Mutu Wokha, Ndiye Mukumulonda Londa Bwanji Celeb Wathuyo? Ameneyo Si Gay Kuti Akakhale Wopanda Chilako Lako. Mwina Mukungofunako Ndalama Malinga Ndi January Wabvuta Uyu. Joe Saizi Ikukana Mutu Wokha Ndiwo Udasuzumirako Mtayeni
kkkkkkk kodi ameneyu ndi mr musican#gwaladi? kkkkkkkkkkk
ndalephera kufotokozaaa! kuti uyu simwana ayii! kkkk me singn’ [Davies & Edgar]
Kaoneka mulungu wakwia nanu khaladwe lake ili ,muti tizimupepha chauta
Unu amene mukuweluzilatu azanu padziko lapasinu Mulungu alinanu ntchito BASI NDAMALIZA
Angomukhumba moti azikamba zama gay akulimbana ndimusangalasi wathuyi kusowa zochita eti komanso galu amapita kumene kuli galu wamkazi osati galu wamuna kupita kumene kuli galu wamuna ndiye musadane naye munthuyi akulongosola mmene zimakhalira sizama gay zo
Sadagwirire koma kuti amupeza ali ndi bwenzi lake
Hahahahahaha bwanji gwaradi
Gwaladi ndi Kanene wa ku malawi. But vocabulary yavuta; its not raping please ndi chibwenzitu.
anthu osauka inu ,,, kusiya kumapukuta madazi onunkhawo , mukulimbana ndi mphawi nzanga uyu zisiru zawathu , munthu wazaka 14 umwana wake ulipati ngakhale amadazi inu mutha kumunyenga kma kumangoti em emm kma mukanakhala inu pansana panu
Gwaladi anatani? ?? Aysha Tawakali
Sorry not in watsp for a while gat problem
Ai km
Koma Mvulayi Mukuyiwona Bwanji Guys Mulungu Watidalitsatu
Sured mani, watidalitsadi wam’mwambayo, groly be 2 Him
Aaaaa za ziiiiiii,,,Kodi guys ali ndi Charger cha NOKIA ndani
Kodi mkaziyo wavulala?musataye nthawi ndichibwenzi icho
Kkkk
Kkkkkkkkk msiyen celeb waku muz
Ee! Adzingoona milandu ina uu kudupha(gay)
Koma Kungowina Mulandu Umenewu,mukonzekere Single Track Yovuta Heavy
Kodi amphunzitsi mwatanitso kodi?? Malangizo mumagawa inu nomwetu! Zotsakhala bwino nanga!!..
Gwalad nd Gwaland…
Tamusiyeni poti ndi iyeyu nanga mp wa udf uja ilowaso liti
kodi malamuro ati chani? ngati anagwirila let him face the law
malamulo agwire ntchito posatengera kuti kaya ndindani
Mwaulemu mumusiye mbuyacheyo ndisaputanepo apaaa
Pepani mr gwaladi iyi tingoti ndiminyama basi ,kodi asangalase dziko lamalawi ndani ,uyu ndilangizi wa Africa ,
Mmmmmmm a Malawi kukakamila zinthu zochepa kulephela kuthana ndi mavuto akuluakulu Gwaladi kwake ndi kusangalatsa anthu basi.
A kumamusaka musiyen chinali chibwezi
Atron zoona ukunenazi
I c this regime of #Peter iz focussing things that will take us nowhere. Plz leave #Gwalad alone
musiyeni mzanu alibe kalikonse chonde
mutayeni!
Ooooooo!!!.. Kansi Aliko Kwachimweene Kanene?. Inenimati Nikunokokha Tili Ndi Kanene Chidyamakanda. All the Best Amweene!..
Ndimatenda ake ameneyo
Chifukwa chokuti anali nsikana akanagwilirila mwamuna nzake akanandila thumba la makobidi mkupulumukanso ku chi mlanducho mdzina la #UFULU kkk koooomaaaaaaaaaa #KAYAAAAAAAAAAA
Malawi dnt be stupid,,,u r duin dis just bcoz he dnt hv a nem n money,,,fuck dem
Akanakhala mwana wanu mukanatani? Ngati anagwiriradi akuyenera kulangidwa iyaa
kkkkkkkkkk koma kumeneko mmalo mot muthetse umphawi mukulimbana ndi za ziii…..k
indeed this regime is practising capitalism, what a wonderful regime like this one whch i had never seen
Zaiiiiiiiiiiiiiiiii
Kkkkkkkkkkk koma guyz
Sweka basi mwene gwaladi akunamizila
Kodi pano boma likungokakamira Malawi nzangayu bwanji musiyeni
Mwangomupansa minyama Gwaladi…atuluke bssi alowe amathanyulawo
Guys m’malo momawona zachituko mukulimbana ndi za anthu osauka bwanji?M’tundu Wa Malawi siuzatukuka guys .
Musiyeni ayende zake Gwaladi anagwirizana
Mxm ,One size fits ol
Angowona kumulakwila khenadhuwelha alhomwe
achina trapency busy ndizamatanyura,ma mp anagwdwa zzomwez koma awa siawwo akuwakakamra mbuzzz
Mwangomupatsa minyama Gwaladi!
JUDGE Damson Banda is one of the corrupt judges. He was at Balaka. He is no good. He does not deserve to be a judge. I believe these judges need to have a Degree. Look around atumbuka ambili ndi ma judge. WAKWITHU.
Panyapanu athu nose gwarad amagidwe warakwa sizausiru mukukambazo
No gd,mpaka kutukwana man
All the best gwaradi agaluwa angofuna kukuonongera mbiri
akapezeka olakwa,mmangeni basi
vutolanu chan? musiyeni munthu osalakwayu!
Musieni Gwaladi,, iyetu anakwatila mkazi uja amat pepani ndalama zanu ndizosakwanira waku TNM
Lets talk of 120 delegates u took to USA, how many kwachas, millions,billions u squandered for that trip? Then u hav forgotten those stupid things,now u want to take part 4 Gwaladi’s case.How stupid r u? If u r not part of solution, u r part of the problem!
Kkk Inuso Munangokula Mutu Koma Nzeru Mulibe Nanga Comment Yanuyo Ikugwirizana Bwanji Ndi Nkhaniyi Hahaha, Xool SiMkalasi Moka Eti, Kkkk
Kkkkkkkkkkk koma Cosmas Goman
mbalame #cosmas_gonani u think de comment doesnt tally? sukulu yake iti yomwe mwaphunzirayo!! zazii
14 yrs ndi mwana?tamaganizani nanu inu.munthu okutha nsikhu ngati ameneyu angakhale mwana?
Zanziiiiiiiiiiiiiii
Leave my celeb alone please
kkkkkkkkk he is going my dear….
Kkkkkk zisatero nanga atilangiza ndani
Kkkk serious a hope
Bwanji ma gayezimu
ngati 2 amalowa mu 1 opanda vuto palibe mlandu kaa kkkk last days yaweh hav mercy on us
Zaziiiii m’malo molimba ndi acash gate mukulimbana ndi kapolo ngati ameneyo.inu mbuzi za anthu nonse
Si bho koma
Kkkkkkkkklkkkkkkkkkk tangomsiyani uyo ndiwamasiye koma makolo alinawo
Nawenso adimin uziyankhula bwino streat perfomer
Koma akanakhala awa ali ndi maina kale ku khothi wa bwenzi mlandu utatha tsiku loyamba lomwelija…mmm dziko lokondera ilo
Ndikungokupemphaniko inu a Malawi24 Mutifufuzilleko nkhani ya anthu aja anagwidwa akupanga za u GAY aja Ku Lilongwe kuti zili pati…tikudabwa nazo zangoti ziii…
Man Anthu amene aja anatulutsidwa pano ndi mfulu
#Chithumba,alibe ufulu amenewaja ikubwera nthawi yawo…
14yrs old? Simwana ameneyo ankamvana nd gwalad kanayamba kuonera zolaula mufon kali nd zaka 10 gwalad siolakwa kungoti tatskanati uhule kususukira chipisi komaso salad.Mp wina anapangaso zofoila zomwez koma mulandu wake sizkudziwikaso
zopusa,zauchitsiru,zaziii, basi mawa mafile mmanja nkhani yake imeneyi kulibe mlandu wina kuposa umenewo. Ife tinayiwala zimenezo
Panyopanu nonse Gwaladi sadalakwe,bwana Gwaladi musadande zazing’ono zimenezo
Mr chikwapa fear GOD When your staying, up to use obsacen lagauge. The Fear of the Lord is begenning of the wisdom.
Tumbocid
Mwasowa chochita eti mlandu wa kalekale mukufuna kumudyela .
Kkkkkkkk
Ngati anatuluka General kanene ndiye gwaladi alekeranji kutuluka mukunamatu inuyo.
kodi general anatuluka?
Eya anatuluka
gwaladi ndi celeb,,ndi owina wina mukungoononga tchelete wanu
Not fair…mkazi anapita ekha mnumba mwa joe,means chinali chibwenzi…si boh.
kkkkkkk mlimi ameneyi basi adyeledwe isaaa
hahaha ke masepa fela
The TUMBOCID hit maker hired lawyer,,,,,Gwaladi ali ndalama mpaka kugula Lawyer????????????????????
Osamalimbana ndi anthu anati bela ndalamawa bwanj
Boma ikufuna kuiyamwa yowondawonda futseck
Kkkk Joe gwaladi ndiwoimba kuyambila kale eee!!
Kkkkkkkkkkk
Mesa adawina kale mulanduwu
Kkkk!
just because is streetboy gwaladi. Mp kaliati did the same but now he is a free man although the case was withdrawn by the complainant imagine if those sued gwaladi withdrew the case today what will those noisy N.G.O.s do? Definetely they will take an injunction so that the case should go on. I cry for my fellow low class. Gwaladi afotokoze bwanji kuti amene uja simwana kapena apange demonstrate?
nanga onyengana okhaokha aja mlandu uliko liti?
This z no sense gyz
Prisons r no longer places for lomwe-belt pple. Ask yourself where is christopher naphiyo
Ife tidayiwala kalekale zimenezo.
Nanga aja Amathanyula aja ma (gay) muwazenga liti Mulandu??? Zafodya basi….
zisiyeni zagwaladizo, anthu akulira mvula.
LIES GO FASTER DAN TRUTH….lol
aaaaa demeti milandu ya anthu osauka kukakamilidwa eish
Cholinga mumubere basi agalu inu koma munyatu munya! Mumusiye mwana wakwathu apo ai mlanduwo upite kukhot lalikulu pa dziko lapansi ICC
vutondlakuti dziko ndilokondela mun2 osauka akaba nkhuku amamulanga kuposawauba galimoto zopusa basi
musiyen Gwaladi inu!! why is this system so heartles?
koma anaswa mphika wamwanayo?
Mukumusatabe kod?Ndisamveso zimenezo mukufuna mumubeleso kawiri ?
Gwalad Siolakwa bt angofuna kumuonongela mbiri .
takakambani za cashgate zithe musalimbane ndi izi
Allthe best my home
yu waist time with reporting negative stories why cant yu talk good about others??
Chamba et….
ine nafa mbewa!ukayimbira ku jail! kkkk
Kkkkkkkkk tsono m’mansomo ati anatola ma garasi
kkkkk koma iyeyu mpaka kugwilira?zinamuvuta bwanji?