Gwaladi case resumes tomorrow

Advertisement
Joe Gwaladi
Joe Gwaladi
Gwaladi: His case continues in court.

The court case against Malawi’s popular street-performer, Joe Gwaladi, in which he is accused of  raping a 14 year-old girl will resume tomorrow at Phalombe First Grade Magistrate Court.

Gwaladi was arrested by Phalombe Police in May last year on suspicion that he defiled a 14 year-old girl. The Tumbocid hit maker hired lawyer Chancy Gondwe and he was released on court bail. He was ordered to pay a bail bond of K100,000 by first grade magistrate Damson Banda.

Phalombe Police Spokesperson, Augustus Nkhwazi, confirmed to the media last week that the case will be back in court on January 19.

However, the publicist did not explain why the case is dragging saying it is being handled by state prosecutors.

The “Ndikanadziwa sindinakapanga” star, denied the charges of defilement levelled against him.

Advertisement

153 Comments

 1. Oimba mukamapanga ubwenzi ndi wana muzionetsetsa fwa ndinu anthu amodzi amene mumatsatidwa kwambiri. Komanso a gwaladi mwanyanya kuimba zolaula mpake ake sakukaika kuti munagwiririra

 2. Abale’ Kodi ati Gwaladi atangoilowesa mtsikanayu amalilira kuti asachotse? Kkkkkk! Mwana amatero? Ifetu ATcheya anatiuza kuti Mwana wa mkazi akangomera mabere pa mtima basi wakwana ameneyo! Kkkkkk mmasuleni munthu according to Atcheya Theorem!!!

 3. Uwu nde usilu mukufuna kusautsa munthu ndi nkhani yogula maliseche mesa iye amadya ndalama yake, Kodi nanu aboma mukulephera kuzenga mlandu aCASHGATE, okuba Subsidy tools , NDUNA zogwirira zija zafodya basi iZAPSATU COURT kumalawi kuno

 4. koma akhwaka nyuwanho tamusyen mfana wakumuz kwathuyo,It means tzgonana amuna okhaokha akaz tsamagonenawo???? mundyankhe ndsayambe kukumba munsewu!!!!

 5. momwe amalowetsa kwamanayo imawawa or amava bwino ngati amava kuwawa agwaladi asakane anagwiririla ngati amava bwino nanga chomangilaso ndichani poti amafilana boo?

 6. Komatu Joe Adakamba Kale Kuti Udangolowa Mutu Wokha, Ndiye Mukumulonda Londa Bwanji Celeb Wathuyo? Ameneyo Si Gay Kuti Akakhale Wopanda Chilako Lako. Mwina Mukungofunako Ndalama Malinga Ndi January Wabvuta Uyu. Joe Saizi Ikukana Mutu Wokha Ndiwo Udasuzumirako Mtayeni

 7. Angomukhumba moti azikamba zama gay akulimbana ndimusangalasi wathuyi kusowa zochita eti komanso galu amapita kumene kuli galu wamkazi osati galu wamuna kupita kumene kuli galu wamuna ndiye musadane naye munthuyi akulongosola mmene zimakhalira sizama gay zo

 8. anthu osauka inu ,,, kusiya kumapukuta madazi onunkhawo , mukulimbana ndi mphawi nzanga uyu zisiru zawathu , munthu wazaka 14 umwana wake ulipati ngakhale amadazi inu mutha kumunyenga kma kumangoti em emm kma mukanakhala inu pansana panu

 9. kodi malamuro ati chani? ngati anagwirila let him face the law
  malamulo agwire ntchito posatengera kuti kaya ndindani

 10. Chifukwa chokuti anali nsikana akanagwilirila mwamuna nzake akanandila thumba la makobidi mkupulumukanso ku chi mlanducho mdzina la #UFULU kkk koooomaaaaaaaaaa #KAYAAAAAAAAAAA

 11. JUDGE Damson Banda is one of the corrupt judges. He was at Balaka. He is no good. He does not deserve to be a judge. I believe these judges need to have a Degree. Look around atumbuka ambili ndi ma judge. WAKWITHU.

 12. Lets talk of 120 delegates u took to USA, how many kwachas, millions,billions u squandered for that trip? Then u hav forgotten those stupid things,now u want to take part 4 Gwaladi’s case.How stupid r u? If u r not part of solution, u r part of the problem!

  1. Kkk Inuso Munangokula Mutu Koma Nzeru Mulibe Nanga Comment Yanuyo Ikugwirizana Bwanji Ndi Nkhaniyi Hahaha, Xool SiMkalasi Moka Eti, Kkkk

 13. Koma akanakhala awa ali ndi maina kale ku khothi wa bwenzi mlandu utatha tsiku loyamba lomwelija…mmm dziko lokondera ilo

 14. Ndikungokupemphaniko inu a Malawi24 Mutifufuzilleko nkhani ya anthu aja anagwidwa akupanga za u GAY aja Ku Lilongwe kuti zili pati…tikudabwa nazo zangoti ziii…

 15. 14yrs old? Simwana ameneyo ankamvana nd gwalad kanayamba kuonera zolaula mufon kali nd zaka 10 gwalad siolakwa kungoti tatskanati uhule kususukira chipisi komaso salad.Mp wina anapangaso zofoila zomwez koma mulandu wake sizkudziwikaso

 16. zopusa,zauchitsiru,zaziii, basi mawa mafile mmanja nkhani yake imeneyi kulibe mlandu wina kuposa umenewo. Ife tinayiwala zimenezo

 17. The TUMBOCID hit maker hired lawyer,,,,,Gwaladi ali ndalama mpaka kugula Lawyer????????????????????

 18. just because is streetboy gwaladi. Mp kaliati did the same but now he is a free man although the case was withdrawn by the complainant imagine if those sued gwaladi withdrew the case today what will those noisy N.G.O.s do? Definetely they will take an injunction so that the case should go on. I cry for my fellow low class. Gwaladi afotokoze bwanji kuti amene uja simwana kapena apange demonstrate?

 19. Cholinga mumubere basi agalu inu koma munyatu munya! Mumusiye mwana wakwathu apo ai mlanduwo upite kukhot lalikulu pa dziko lapansi ICC

Comments are closed.