Promise Kamwendo tsopano ndi wa Wanderers
Zitasokonekera chaka chatha za ulendo wake obwera ku Mighty Mukuru Wanderers, Promise Kamwendo tsopano lero ndi osewera wa timuyi kutsatira mgwirizano wa zaka zitatu omwe atsimikizirana lero. Mighty Mukuru Wanderers yatsimikiza za nkhaniyi kudzera mu… ...