‘Kulibe mpungwepungwe mu mgwirizano wa Tonse’
A kunyumba ya boma atsutsa mphekesera zoti mu mgwirizano wa Tonse muli mpungwepungwe. Nkhaniyi ikutsatira manong'onong'o omwe akhala akumveka makamaka pamasamba amchezo oti akuluakulu azipani zomwe zili mugwirizanowu sakumwerana madzi kaamba kosepmhana chichewa pazinthu zina.… ...