Zina ukamva: Bambo adula mutu wa nkazi ndi mwana kenaka nkudzikhweza
Bambo wa zaka 27 m’boma la Karonga wadabwitsa anthu pomwe wadula mutu wa nkazi komaso mwana wake kenakaso naye nkudzimangilira. Izi ndi malingana ofalitsa nkhani pa polisi ya Karonga a George Mulewa omwe azindikira bamboyu… ...