Wathilidwa unyolo kamba kopezeka ndi ma K5,000 okwana K240,000 achinyengo
A Maxwell James a zaka 23 zakubadwa akusungidwa mchitokosi cha apolisi ku Phalombe kamba kopezeka ndi ndalama zachinyengo zokwana K240,000. Nkhani yonse ikuti pa 9 December a James adapita ku msika wawukulu wa Mulomba komwe… ...