Apolisi ayamba kumanga omwe anatchingira nsewu Chakwera ku Blantyre
Malipoti osatsimikizika akusonyesa kuti apolisi munzinda wa Blantyre amanga anthu awiri powaganizira kuti anali nawo mu gulu la anamalira omwe anatchingira nsewu mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pa mphambano… ...