Apolisi anjata mayi kamba kotentha ndikuvulaza mwana wake
A polisi m’boma la Dowa akusunga mchitolokosi a Chimwemwe Kayera azaka 35 zakubadwa, kamba kowaganizira kuti anawotcha ndi kuvulaza mwana wawo wamamuna wa zaka khumi ndi ziwiri (12). Mneneri wa Polisi ya Dowa a Seageant… ...